Eksodo 4:3 - Buku Lopatulika3 Ndipo ananena Iye, Iponye pansi. Naiponya pansi, ndipo inasanduka njoka; ndipo Mose anaithawa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ndipo ananena Iye, Iponye pansi. Naiponya pansi, ndipo inasanduka njoka; ndipo Mose anaithawa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Chauta adamuuza kuti, “Taiponya pansi.” Mose ataiponya pansi ndodoyo, idasanduka njoka, iye nkuithaŵa njokayo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Yehova anati, “Tayiponya pansi.” Mose anayiponya pansi ndipo inasanduka njoka ndipo anayithawa. Onani mutuwo |