Eksodo 4:2 - Buku Lopatulika2 Ndipo Yehova ananena naye, Icho nchiyani m'dzanja lako? Nati, Ndodo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ndipo Yehova ananena naye, Icho nchiyani m'dzanja lako? Nati, Ndodo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Chauta adafunsa Moseyo kuti, “Kodi nchiyani chili m'manja mwakocho?” Mose adayankha kuti, “Ndodo.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Ndipo Yehova anamufunsa nati, “Nʼchiyani chili mʼdzanja lakolo?” Mose anayankha kuti, “Ndodo.” Onani mutuwo |