Eksodo 4:26 - Buku Lopatulika26 Pamenepo anati mkaziyo, Mkwati wamwazi iwe, chifukwa cha mdulidwe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 Pamenepo anati mkaziyo, Mkwati wamwazi iwe, chifukwa cha mdulidwe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 Choncho Chauta adamleka Mose osamupha. Ndiye pamene Zipora adanena kuti, “Ndiwe mkwati woomboledwa ndi magazi,” chifukwa cha kuumbalako. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 Choncho Yehova anamuleka Mose wosamupha. Pa nthawiyo, Zipora anati, “Mkwati wa magazi,” ponena za mdulidwe. Onani mutuwo |