Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Eksodo 4:26 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

26 Choncho Yehova anamuleka Mose wosamupha. Pa nthawiyo, Zipora anati, “Mkwati wa magazi,” ponena za mdulidwe.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

26 Pamenepo anati mkaziyo, Mkwati wamwazi iwe, chifukwa cha mdulidwe.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

26 Pamenepo anati mkaziyo, Mkwati wamwazi iwe, chifukwa cha mdulidwe.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

26 Choncho Chauta adamleka Mose osamupha. Ndiye pamene Zipora adanena kuti, “Ndiwe mkwati woomboledwa ndi magazi,” chifukwa cha kuumbalako.

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 4:26
2 Mawu Ofanana  

Koma Zipora anatenga mwala wakuthwa nachita mdulidwe mwana wake ndipo khungulo analikhudzitsa pa mapazi a Mose. Iye anati “Zoonadi, kwa ine ndiwe mkwati wamagazi.”


Yehova anati kwa Aaroni, “Pita ku chipululu ukakumane ndi Mose.” Iye anapitadi nakakumana ndi Mose pa phiri la Mulungu namupsompsona.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa