Eksodo 4:25 - Buku Lopatulika25 Koma Zipora anatenga mpeni wamwala, nadula khungu la mwana wake, naliponya pa mapazi ake; nati, Pakuti iwe ndiwe mkwati wanga wamwazi. Ndipo Iye anamleka. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 Koma Zipora anatenga mpeni wamwala, nadula khungu la mwana wake, naliponya pa mapazi ake; nati, Pakuti iwe ndiwe mkwati wanga wamwazi. Ndipo Iye anamleka. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Koma Zipora adatenga mwala wakuthwa, naumbala mwana wake, ndipo khungulo adalikhudzitsa m'miyendo mwa Mose. Kenaka Ziporayo adati, “Zoonadi, iwe ndiwe mkwati woomboledwa ndi magazi.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Koma Zipora anatenga mwala wakuthwa nachita mdulidwe mwana wake ndipo khungulo analikhudzitsa pa mapazi a Mose. Iye anati “Zoonadi, kwa ine ndiwe mkwati wamagazi.” Onani mutuwo |