Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Eksodo 4:25 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

25 Koma Zipora anatenga mwala wakuthwa nachita mdulidwe mwana wake ndipo khungulo analikhudzitsa pa mapazi a Mose. Iye anati “Zoonadi, kwa ine ndiwe mkwati wamagazi.”

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

25 Koma Zipora anatenga mpeni wamwala, nadula khungu la mwana wake, naliponya pa mapazi ake; nati, Pakuti iwe ndiwe mkwati wanga wamwazi. Ndipo Iye anamleka.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

25 Koma Zipora anatenga mpeni wamwala, nadula khungu la mwana wake, naliponya pa mapazi ake; nati, Pakuti iwe ndiwe mkwati wanga wamwazi. Ndipo Iye anamleka.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

25 Koma Zipora adatenga mwala wakuthwa, naumbala mwana wake, ndipo khungulo adalikhudzitsa m'miyendo mwa Mose. Kenaka Ziporayo adati, “Zoonadi, iwe ndiwe mkwati woomboledwa ndi magazi.”

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 4:25
6 Mawu Ofanana  

Mwamuna aliyense amene adzakhala wosachita mdulidwe adzachotsedwa pakati pa anthu ake chifukwa sanasunge pangano langa.”


Potukwana, Simeiyo amati, “Choka iwe, choka iwe, munthu wopha anthu, munthu wachabechabe iwe!


Mose atamubweza Zipora, mkazi wake, Yetero, mpongozi wake anamulandira


Mose anavomera kukhala ndi Reueli, ndipo anamupatsa Zipora kuti akhale mkazi wake.


Choncho Yehova anamuleka Mose wosamupha. Pa nthawiyo, Zipora anati, “Mkwati wa magazi,” ponena za mdulidwe.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa