Eksodo 4:24 - Buku Lopatulika24 Ndipo kunali panjira, kuchigono, Yehova anakomana naye, nafuna kumupha. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201424 Ndipo kunali panjira, kuchigono, Yehova anakomana naye, nafuna kumupha. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa24 Pambuyo pake Chauta adakumana naye Mose pa njira pa malo a chigono, nafuna kumupha. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero24 Pambuyo pake Mose ali mʼnjira, pamalo wogona, Yehova anakumana naye, ndipo anafuna kumupha. Onani mutuwo |