Eksodo 4:23 - Buku Lopatulika23 Ndipo ndanena ndi iwe, Mlole mwana wanga amuke, kuti anditumikire Ine; koma wakana kumlola kuti asamuke; taona, Ine ndidzamupha mwana wako wamwamuna, mwana wako woyamba. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Ndipo ndanena ndi iwe, Mlole mwana wanga amuke, kuti anditumikire Ine; koma wakana kumlola kuti asamuke; taona, Ine ndidzamupha mwana wako wamwamuna, mwana wako woyamba. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Choncho ndikukuuza kuti umlole mwana wanga apite akandipembedze Ine. Tsono iweyo ukakana, Ine ndidzapha mwana wako wamwamuna wachisamba.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Choncho ndikuti, ‘Mulole mwana wanga apite kuti akandipembedze. Koma ngati ukana, Ine ndidzapha mwana wako wachisamba.’ ” Onani mutuwo |