Eksodo 4:17 - Buku Lopatulika17 Ndipo ukaigwire m'dzanja lako ndodo iyi, imene ukachite nayo zizindikirozo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Ndipo ukaigwire m'dzanja lako ndodo iyi, imene ukachite nayo zizindikirozo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Utenge ndodo ili m'manja mwakoyo, ukachite nayo zozizwitsa ndodo imeneyo.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Koma utenge ndodo imene ili mʼdzanja lakoyo kuti ukachite nayo zizindikiro zozizwitsa.” Onani mutuwo |