Eksodo 4:16 - Buku Lopatulika16 Ndipo iye adzakulankhulira iwe kwa anthu; ndipo kudzatero, kuti iye adzakhala kwa iwe ngati m'kamwa, ndi iwe udzakhala kwa iye ngati Mulungu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Ndipo iye adzakulankhulira iwe kwa anthu; ndipo kudzatero, kuti iye adzakhala kwa iwe ngati m'kamwa, ndi iwe udzakhala kwa iye ngati Mulungu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Iye azikalankhula kwa anthu m'malo mwako. Adzakhala wokulankhulira, ndipo iweyo udzakhala ngati Mulungu ndiwe kwa Aroni. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Iye akayankhula kwa anthu mʼmalo mwako. Iye adzakhala wokuyankhulira ndipo iweyo udzakhala ngati Mulungu kwa iye. Onani mutuwo |