Eksodo 39:16 - Buku Lopatulika16 Anapanganso zoikamo ziwiri zagolide, ndi mphete ziwiri zagolide; naika mphete ziwirizo pansonga ziwiri za chapachifuwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Anapanganso zoikamo ziwiri zagolide, ndi mphete ziwiri zagolide; naika mphete ziwirizo pa nsonga ziwiri za chapachifuwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Adapanganso zoikamo zake ziŵiri zagolide zonga maluŵa, ndiponso mphete ziŵiri, ndipo adalumikiza mphete ziŵirizo ku nsonga zake zapamwamba za chovala chapachifuwacho. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Anapanganso zoyikamo zake zagolide ndi mphete ziwiri zagolide, ndipo anamangirira mphetezo pa ngodya ziwiri za chovala chapachifuwa. Onani mutuwo |