Eksodo 39:16 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Anapanganso zoyikamo zake zagolide ndi mphete ziwiri zagolide, ndipo anamangirira mphetezo pa ngodya ziwiri za chovala chapachifuwa. Onani mutuwoBuku Lopatulika16 Anapanganso zoikamo ziwiri zagolide, ndi mphete ziwiri zagolide; naika mphete ziwirizo pansonga ziwiri za chapachifuwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Anapanganso zoikamo ziwiri zagolide, ndi mphete ziwiri zagolide; naika mphete ziwirizo pa nsonga ziwiri za chapachifuwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Adapanganso zoikamo zake ziŵiri zagolide zonga maluŵa, ndiponso mphete ziŵiri, ndipo adalumikiza mphete ziŵirizo ku nsonga zake zapamwamba za chovala chapachifuwacho. Onani mutuwo |