Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Eksodo 39:17 - Buku Lopatulika

17 Ndipo anamanga maunyolo awiri opota agolide pa mphete ziwiri pansonga za chapachifuwa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

17 Ndipo anamanga maunyolo awiri opota agolide pa mphete ziwiri pa nsonga za chapachifuwa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

17 Tsono zingwe ziŵiri zagolide adazilumikiza ku mphete ziŵiri zija,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

17 Anamangirira timaunyolo tiwiri tagolide tija pa mphete za pa ngodya pa chovala chapachifuwacho.

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 39:17
3 Mawu Ofanana  

ndi maunyolo awiri a golide woona; uwapote ngati zingwe, ntchito yopota; numange maunyolo opotawo pazoikamo.


Anapanganso zoikamo ziwiri zagolide, ndi mphete ziwiri zagolide; naika mphete ziwirizo pansonga ziwiri za chapachifuwa.


Ndi nsonga zake ziwiri zina za maunyolo awiri opotawo anazimanga pa zoikamo ziwiri, nazimanga pa zapamapewa za efodi, m'tsogolo mwake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa