Eksodo 39:10 - Buku Lopatulika10 Ndipo anaika pomwepo mizere inai ya miyala; mzere wa odemu, pitida, ndi bareketi, ndiyo ya mzere woyamba. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ndipo anaika pomwepo mizere inai ya miyala; mzere wa odemu, pitida, ndi bareketi, ndiyo ya mzere woyamba. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Tsono adaikapo mizere inai ya miyala yokongola. Pa mzere woyamba adaika miyala ya rubi, topazi ndi garaneti. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Kenaka anayikapo mizere inayi ya miyala yokongola kwambiri. Mzere woyamba anayika miyala ya rubi, topazi ndi berili; Onani mutuwo |