Eksodo 39:9 - Buku Lopatulika9 Chinakhala chaphwamphwa; anachiomba chapachifuwa chopindika; utali wake dzanja limodzi, ndi kupingasa kwake dzanja limodzi, chinakhala chopindika. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Chinakhala chaphwamphwa; anachiomba chapachifuwa chopindika; utali wake dzanja limodzi, ndi kupingasa kwake dzanja limodzi, chinakhala chopindika. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Kutalika kwake kwa chovala chapachifuwacho kunali masentimita 23, muufupi mwakenso masentimita 23, ndipo chinali chopinda paŵiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Kutalika kwake kunali kofanana mbali zonse, mulitali masentimita 23, mulifupi masentimita 23, chinali chopinda pawiri. Onani mutuwo |