Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Eksodo 39:9 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

9 Kutalika kwake kunali kofanana mbali zonse, mulitali masentimita 23, mulifupi masentimita 23, chinali chopinda pawiri.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

9 Chinakhala chaphwamphwa; anachiomba chapachifuwa chopindika; utali wake dzanja limodzi, ndi kupingasa kwake dzanja limodzi, chinakhala chopindika.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

9 Chinakhala chaphwamphwa; anachiomba chapachifuwa chopindika; utali wake dzanja limodzi, ndi kupingasa kwake dzanja limodzi, chinakhala chopindika.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

9 Kutalika kwake kwa chovala chapachifuwacho kunali masentimita 23, muufupi mwakenso masentimita 23, ndipo chinali chopinda paŵiri.

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 39:9
2 Mawu Ofanana  

Kenaka anayikapo mizere inayi ya miyala yokongola kwambiri. Mzere woyamba anayika miyala ya rubi, topazi ndi berili;


Iwo anapanga chovala chapachifuwa mwaluso kwambiri. Anachipanga ngati efodi pogwiritsa ntchito golide, nsalu yamtundu wa mtambo, yapepo, yofiira, yofewa yosalala ndi yolukidwa bwino.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa