Eksodo 39:11 - Buku Lopatulika11 Ndi mzere wachiwiri wa nofeki, safiro, ndi yahalomu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Ndi mzere wachiwiri wa nofeki, safiro, ndi yahalomu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Pa mzere wachiŵiri adaika miyala ya emeradi, safiro ndi daimondi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 mzere wachiwiri anayikapo miyala ya emeradi, safiro ndi dayimondi; Onani mutuwo |