Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Eksodo 39:10 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

10 Kenaka anayikapo mizere inayi ya miyala yokongola kwambiri. Mzere woyamba anayika miyala ya rubi, topazi ndi berili;

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

10 Ndipo anaika pomwepo mizere inai ya miyala; mzere wa odemu, pitida, ndi bareketi, ndiyo ya mzere woyamba.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

10 Ndipo anaika pomwepo mizere inai ya miyala; mzere wa odemu, pitida, ndi bareketi, ndiyo ya mzere woyamba.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

10 Tsono adaikapo mizere inai ya miyala yokongola. Pa mzere woyamba adaika miyala ya rubi, topazi ndi garaneti.

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 39:10
6 Mawu Ofanana  

Nzeru sungayiyerekeze ndi miyala ya topazi ya ku Kusi; nzeru singagulidwe ndi golide wabwino kwambiri.


Miyalayo ikhalepo khumi ndi iwiri, uliwonse kuyimira dzina limodzi la ana a Israeli. Mwala uliwonse uzokotedwe ngati chidindo dzina limodzi la mafuko khumi ndi awiri a Israeli.


mzere wachiwiri anayikapo miyala ya emeradi, safiro ndi dayimondi;


Kutalika kwake kunali kofanana mbali zonse, mulitali masentimita 23, mulifupi masentimita 23, chinali chopinda pawiri.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa