Eksodo 3:11 - Buku Lopatulika11 Koma Mose anati kwa Mulungu Ndine yani ine kuti ndipite kwa Farao, ndi kuti nditulutse ana a Israele mu Ejipito? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Koma Mose anati kwa Mulungu Ndine yani ine kuti ndipite kwa Farao, ndi kuti nditulutse ana a Israele m'Ejipito? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Apo Mose adafunsa kuti, “Kodi ndine yani ine, kuti ndingapite kwa Farao ndi kukatulutsa Aisraele ku Ejipito?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Koma Mose anafunsa Mulungu, “Ine ndine yani kuti ndipite kwa Farao ndi kukatulutsa Aisraeli mʼdziko la Igupto?” Onani mutuwo |