Eksodo 27:7 - Buku Lopatulika7 Ndipo apise mphiko m'mphetezo kuti mphikozo zikhale pa mbali ziwiri za guwa la nsembe polinyamula. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Ndipo apise mphiko m'mphetezo kuti mphikozo zikhale pa mbali ziwiri za guwa la nsembe polinyamula. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Ponyamula guwalo, mphikozo azizipisa m'mphete za pa mbali ziŵiri za guwalo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Pamene mukunyamula guwalo, muzilowetsa nsichizo mʼmphetemo mbali zonse ziwiri za guwalo. Onani mutuwo |