Eksodo 27:6 - Buku Lopatulika6 Ndipo upangire guwa la nsembe mphiko, mphiko za mtengo wakasiya, ndi kuzikuta ndi mkuwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Ndipo upangire guwa la nsembe mphiko, mphiko za mtengo wakasiya, ndi kuzikuta ndi mkuwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Upange mphiko ya mtengo wa kasiya yonyamulira guwalo, ndipo uikute ndi mkuŵa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Upange nsichi zamtengo wa mkesha ndipo uzikutire ndi mkuwa. Onani mutuwo |