Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Eksodo 27:5 - Buku Lopatulika

5 Nuwaike pansi pa khoma lamkati la guwa la nsembelo posungulira, kuti malukidwe alekeze pakati pa guwa la nsembelo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 Nuwaike pansi pa khoma lamkati la guwa la nsembelo posungulira, kuti malukidwe alekeze pakati pa guwa la nsembelo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Uike sefayo m'munsi mwake mwa chibumi cha guwalo, ndipo ilekeze pakati pa guwalo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 Uyike sefayo mmunsi mwa khoma la guwa lansembelo, ndipo ilekezere pakati pa guwa lansembelo.

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 27:5
4 Mawu Ofanana  

Ndipo ulipangire sefa, malukidwe ake ndi amkuwa; nupange pa malukidwewo ngodya zake zinai mphete zinai zamkuwa.


Ndipo upangire guwa la nsembe mphiko, mphiko za mtengo wakasiya, ndi kuzikuta ndi mkuwa.


Ndipo anapangira guwa la nsembelo sefa, malukidwe ake nja mkuwa, pansi pa khoma lamkati lake wakulekeza pakati pake.


Ndi kuyambira kunsi kwake kunthaka, kufikira phaka lamunsi, mikono iwiri; ndi kupingasa kwake mkono umodzi; ndi kuyambira phaka laling'ono kufikira phaka lalikulu mikono inai; ndi kupingasa kwake mkono.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa