Eksodo 27:4 - Buku Lopatulika4 Ndipo ulipangire sefa, malukidwe ake ndi amkuwa; nupange pa malukidwewo ngodya zake zinai mphete zinai zamkuwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ndipo ulipangire sefa, malukidwe ake ndi amkuwa; nupange pa malukidwewo ngodya zake zinai mphete zinai zamkuwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Upangenso chitsulo chamkuŵa choboolaboola ngati sefa. Pa ngodya zake za chitsulocho upange mphete zamkuŵa zonyamulira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Upange sefa yachitsulo chamkuwa ndipo mʼngodya zake zinayizo upangiremo mphete zamkuwa. Onani mutuwo |