Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Eksodo 27:4 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

4 Upange sefa yachitsulo chamkuwa ndipo mʼngodya zake zinayizo upangiremo mphete zamkuwa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

4 Ndipo ulipangire sefa, malukidwe ake ndi amkuwa; nupange pa malukidwewo ngodya zake zinai mphete zinai zamkuwa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

4 Ndipo ulipangire sefa, malukidwe ake ndi amkuwa; nupange pa malukidwewo ngodya zake zinai mphete zinai zamkuwa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

4 Upangenso chitsulo chamkuŵa choboolaboola ngati sefa. Pa ngodya zake za chitsulocho upange mphete zamkuŵa zonyamulira.

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 27:4
6 Mawu Ofanana  

Upange mphete zinayi zagolide ndipo uzimangirire ku miyendo yake inayi ya bokosilo, mbali ina ziwiri ndi mbali inanso ziwiri.


Upange ziwiya zamkuwa izi zogwirira ntchito pa guwalo: miphika yochotsera phulusa, mafosholo, mabeseni owazira magazi, ngowe zokowera nyama ndi zosonkhezera moto.


Uyike sefayo mmunsi mwa khoma la guwa lansembelo, ndipo ilekezere pakati pa guwa lansembelo.


guwa lansembe yopsereza pamodzi ndi sefa yamkuwa, mitengo yake yonyamulira ndi zipangizo zake zonse, beseni losambira lamkuwa ndi miyendo yake;


Iwo anawugwiritsa ntchito popanga matsinde a pa chipata cha tenti ya msonkhano, guwa la mkuwa pamodzi ndi sefa yake ndiponso ziwiya zonse,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa