Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Eksodo 27:6 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

6 Upange nsichi zamtengo wa mkesha ndipo uzikutire ndi mkuwa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

6 Ndipo upangire guwa la nsembe mphiko, mphiko za mtengo wakasiya, ndi kuzikuta ndi mkuwa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

6 Ndipo upangire guwa la nsembe mphiko, mphiko za mtengo wakasiya, ndi kuzikuta ndi mkuwa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

6 Upange mphiko ya mtengo wa kasiya yonyamulira guwalo, ndipo uikute ndi mkuŵa.

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 27:6
7 Mawu Ofanana  

Bokosilo ulikute ndi golide wabwino kwambiri, mʼkati mwake ndi kunja komwe, ndipo upange mkombero wagolide kuzungulira bokosilo.


zikopa za nkhosa zazimuna za utoto wofiira ndi zikopa za akatumbu; matabwa amtengo wa mkesha;


Uyike sefayo mmunsi mwa khoma la guwa lansembelo, ndipo ilekezere pakati pa guwa lansembelo.


Pamene mukunyamula guwalo, muzilowetsa nsichizo mʼmphetemo mbali zonse ziwiri za guwalo.


Upange mphete ziwiri zagolide ndipo uzilumikize ku guwa mʼmunsi mwa mkombero, mphete ziwiri ku mbali zonse ziwiri zoyangʼanana. Mphetozo zizigwira nsichi zonyamulira guwalo.


atawawerenga mwa mafuko ndi mabanja awo, anali 3,200.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa