Eksodo 27:10 - Buku Lopatulika10 ndi nsichi zake makumi awiri, ndi makamwa ao makumi awiri akhale amkuwa; zokowera za nsichi ndi mitanda yake zikhale zasiliva. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 ndi nsichi zake makumi awiri, ndi makamwa ao makumi awiri akhale amkuwa; zokowera za nsichi ndi mitanda yake zikhale zasiliva. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Nsanamira zake 20 ndi masinde ake 20 zikhale zamkuŵa, koma ngoŵe za nsanamirazo, pamodzi ndi mitanda yake, zikhale zasiliva. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Upangenso mizati makumi awiri, matsinde makumi awiri amkuwa, ndi ngowe zasiliva ndi zingwe za mizatiyo. Onani mutuwo |