Eksodo 27:10 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Upangenso mizati makumi awiri, matsinde makumi awiri amkuwa, ndi ngowe zasiliva ndi zingwe za mizatiyo. Onani mutuwoBuku Lopatulika10 ndi nsichi zake makumi awiri, ndi makamwa ao makumi awiri akhale amkuwa; zokowera za nsichi ndi mitanda yake zikhale zasiliva. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 ndi nsichi zake makumi awiri, ndi makamwa ao makumi awiri akhale amkuwa; zokowera za nsichi ndi mitanda yake zikhale zasiliva. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Nsanamira zake 20 ndi masinde ake 20 zikhale zamkuŵa, koma ngoŵe za nsanamirazo, pamodzi ndi mitanda yake, zikhale zasiliva. Onani mutuwo |