Eksodo 26:34 - Buku Lopatulika34 Ndipo uziika chotetezerapo pa likasa la mboni, m'malo opatulika kwambiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201434 Ndipo uziika chotetezerapo pa likasa la mboni, m'malo opatulika kwambiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa34 Uike chivundikiro chija pa bokosi lachipangano ku malo opatulika kopambanawo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero34 Uyike chivundikiro pa bokosi laumboni ku malo wopatulika kwambiri. Onani mutuwo |