Eksodo 26:33 - Buku Lopatulika33 Ndipo uzitchinga nsalu yotchinga pa zokowerazo, nulowetse likasa la mboni kukati kwa nsalu yotchinga; ndipo nsalu yotchingayo idzakugawirani pakati pa malo opatulika ndi malo opatulika kwambiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201433 Ndipo uzitchinga nsalu yotchinga pa zokowerazo, nulowetse likasa la mboni kukati kwa nsalu yotchinga; ndipo nsalu yotchingayo idzakugawirani pakati pa malo opatulika ndi malo opatulika kwambiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa33 Ukoloŵeke nsalu yochingayo ku ngoŵezo ndipo uike bokosi lachipangano lija m'kati momwemo, kuseri kwa nsalu yochingayo. Nsalu yochingayo idzalekanitsa malo opatulika ndi malo opatulika kopambana. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero33 Ukoloweke kataniyo ku ngowe ndipo uyike Bokosi la Chipangano mʼkatimo. Kataniyo idzalekanitse malo wopatulika ndi malo wopatulika kwambiri. Onani mutuwo |