Eksodo 26:35 - Buku Lopatulika35 Nuziika gomelo kunja kwa nsalu yotchinga, ndi choikaponyali pandunji pa gome, pa mbali ya kumwera ya chihema; koma uike gomelo pa mbali ya kumpoto. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201435 Nuziika gomelo kunja kwa nsalu yotchinga, ndi choikapo nyali pandunji pa gome, pa mbali ya kumwera ya Kachisi; koma uike gomelo pa mbali ya kumpoto. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa35 Tebulo lija uliike kunja kwa nsalu yochingayo. Choikaponyale chija uchiike chakumwera kwake kwa chihemacho, mopenyana ndi tebulolo, limene likhale mbali yakumpoto. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero35 Uyike tebulo kunja kwa katani yotchinga cha kumpoto kwa chihema ndipo uyike choyikapo nyale chija kummwera moyangʼanana ndi tebulolo. Onani mutuwo |