Eksodo 26:2 - Buku Lopatulika2 Utali wake wa nsalu yophimba imodzi ndiwo mikono makumi awiri kudza isanu ndi itatu, ndi kupingasa kwa nsalu imodzi ndiko mikono inai; nsalu zonse zikhale za muyeso umodzi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Utali wake wa nsalu yophimba imodzi ndiwo mikono makumi awiri kudza isanu ndi itatu, ndi kupingasa kwa nsalu imodzi ndiko mikono inai; nsalu zonse zikhale za muyeso umodzi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Muutali nsalu iliyonse ikhale mamita 13, ndipo muufupi mwake ikhale pafupi mamita aŵiri. Zonsezo zikhale zofanana. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Nsalu zonse zikhale zofanana. Mulitali mwake zikhale mamita khumi ndi atatu, mulifupi mamita awiri. Onani mutuwo |