Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Eksodo 26:2 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

2 Nsalu zonse zikhale zofanana. Mulitali mwake zikhale mamita khumi ndi atatu, mulifupi mamita awiri.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

2 Utali wake wa nsalu yophimba imodzi ndiwo mikono makumi awiri kudza isanu ndi itatu, ndi kupingasa kwa nsalu imodzi ndiko mikono inai; nsalu zonse zikhale za muyeso umodzi.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

2 Utali wake wa nsalu yophimba imodzi ndiwo mikono makumi awiri kudza isanu ndi itatu, ndi kupingasa kwa nsalu imodzi ndiko mikono inai; nsalu zonse zikhale za muyeso umodzi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

2 Muutali nsalu iliyonse ikhale mamita 13, ndipo muufupi mwake ikhale pafupi mamita aŵiri. Zonsezo zikhale zofanana.

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 26:2
6 Mawu Ofanana  

mfumuyo inawuza mneneri Natani kuti, “Ine pano ndikukhala mʼnyumba yomanga ndi mitengo ya mkungudza, pomwe Bokosi la Mulungu lili mu tenti.”


Davide atakhazikika mʼnyumba yake yaufumu, anawuza mneneri Natani kuti, “Ine pano ndikukhala mʼnyumba yaufumu yomanga ndi mitengo ya mkungudza, pomwe Bokosi la Chipangano la Yehova lili mu tenti.”


“Panga chihema pogwiritsa ntchito nsalu khumi zofewa, zosalala ndi zolukidwa bwino, zobiriwira, zapepo ndi zofiira. Ndipo anthu aluso apete pa nsaluzo Akerubi.


Ulumikize nsalu zisanu kuti ikhale nsalu imodzi. Uchite chimodzimodzi ndi nsalu zisanu zinazo.


Azinyamula makatani a ku chihema, tenti ya msonkhano, zokutira zake ndi zokutira kunja za zikopa za akatumbu, makatani a pa khomo la ku tenti ya msonkhano,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa