Eksodo 26:3 - Buku Lopatulika3 Nsalu zisanu zilumikizane ina ndi inzake; ndi nsalu zisanu zina zilumikizane ina ndi inzake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Nsalu zisanu zilumikizane ina ndi inzake; ndi nsalu zisanu zina zilumikizane ina ndi inzake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Usoke nsalu zisanu kuti zikhale nsalu imodzi, ndipo uchitenso chimodzimodzi ndi nsalu zisanu zinazo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Ulumikize nsalu zisanu kuti ikhale nsalu imodzi. Uchite chimodzimodzi ndi nsalu zisanu zinazo. Onani mutuwo |