Eksodo 24:5 - Buku Lopatulika5 Ndipo anatuma ana a Israele a misinkhu ya anyamata, ndiwo anapereka nsembe zopsereza, naphera Yehova nsembe zamtendere, za ng'ombe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Ndipo anatuma ana a Israele a misinkhu ya anyamata, ndiwo anapereka nsembe zopsereza, naphera Yehova nsembe zamtendere, za ng'ombe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Tsono adatuma Aisraele achinyamata kuti iwoŵa apereke nsembe zopsereza, ndi kupha ng'ombe kuti apereke nsembe zamtendere kwa Chauta. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Kenaka Mose anatuma Aisraeli achinyamata kuti aphe ndi kukapereka kwa Yehova nsembe zopsereza zachiyanjano. Onani mutuwo |