Eksodo 23:9 - Buku Lopatulika9 Usampsinja mlendo; pakuti mudziwa mtima wa mlendo popeza munali alendo m'dziko la Ejipito. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Usampsinja mlendo; pakuti mudziwa mtima wa mlendo popeza munali alendo m'dziko la Ejipito. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 “Musazunze mlendo. Inu nomwe mukudziŵa m'mene amamvera mlendo, poti paja inunso munali alendo ku Ejipito kuja. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 “Usamuzunze mlendo, pakuti inu nomwe mukudziwa mmene amamvera mlendo chifukwa nanunso munali alendo mʼdziko la Igupto. Onani mutuwo |