Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Eksodo 23:10 - Buku Lopatulika

10 Ndipo uzibzala m'munda mwako zaka zisanu ndi chimodzi, ndi kututa zipatso zako;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

10 Ndipo uzibzala m'munda mwako zaka zisanu ndi chimodzi, ndi kututa zipatso zako;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

10 “Muzibzala mbeu zaka zisanu ndi chimodzi m'munda mwanu, ndi kumakolola mbeuzo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

10 “Muzidzala mbewu zanu mʼmunda ndi kumakolola mbewuzo kwa zaka zisanu ndi chimodzi.

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 23:10
6 Mawu Ofanana  

ndipo mitundu ya anthu a m'dziko akabwera nao malonda, ngakhale tirigu, tsiku la Sabata, kutsata malonda, sitidzagulana nao pa tsiku la Sabata, kapena tsiku lina lopatulika, ndi kuti tidzaleka chaka chachisanu ndi chiwiri ndi mangawa ali onse.


koma chaka chachisanu ndi chiwiri uuleke, ugone; kuti aumphawi a anthu a mtundu wako adyemo, ndipo zotsalira nyama zakuthengo zizidye; momwemo uzichita ndi munda wako wampesa, ndi munda wako wa azitona.


Ndipo Yehova ananena ndi Mose m'phiri la Sinai, ndi kuti,


ndi ng'ombe zako, ndi nyama zili m'dziko lako; zipatso zake zonse zikhale chakudya chao.


Ndiponso sunatilowetse m'dziko moyenda mkaka ndi uchi ngati madzi, kapena kutipatsa cholowa cha minda, ndi minda yampesa; kodi udzakolowola amuna awa maso ao: Sitifikako.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa