Eksodo 23:5 - Buku Lopatulika5 Ukaona bulu wa munthu wakudana nawe alikugona pansi ndi katundu wake, ndipo ukadaleka kuthandiza, koma uzimthandiza ndithu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Ukaona bulu wa munthu wakudana nawe alikugona pansi ndi katundu wake, ndipo ukadaleka kuthandiza, koma uzimthandiza ndithu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Bulu wa mdani wako akagwa ndi katundu, usabzole ndi kumsiya, koma umthandize kuti adzuke. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Ngati uwona bulu wa munthu wina amene amakuda atagwa ndi katundu, usamusiye pomwepo, uwonetsetse kuti wamuthandiza. Onani mutuwo |