Eksodo 23:4 - Buku Lopatulika4 Ukakomana ndi ng'ombe kapena bulu wa mdani wako zilinkusokera, uzimbwezera izo ndithu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ukakomana ndi ng'ombe kapena bulu wa mdani wako zilimkusokera, uzimbwezera izo ndithu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 “Ukaona ng'ombe ya mdani wako ikusokera, kapena bulu wake, utenge ukampatse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 “Ngati ukumana ndi ngʼombe kapena bulu wa mdani wako zitasochera, uwonetsetse kuti wazitenga kupita nazo kwa mwini wakeyo. Onani mutuwo |