Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Eksodo 23:4 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

4 “Ngati ukumana ndi ngʼombe kapena bulu wa mdani wako zitasochera, uwonetsetse kuti wazitenga kupita nazo kwa mwini wakeyo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

4 Ukakomana ndi ng'ombe kapena bulu wa mdani wako zilinkusokera, uzimbwezera izo ndithu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

4 Ukakomana ndi ng'ombe kapena bulu wa mdani wako zilimkusokera, uzimbwezera izo ndithu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

4 “Ukaona ng'ombe ya mdani wako ikusokera, kapena bulu wake, utenge ukampatse.

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 23:4
9 Mawu Ofanana  

Ngati mdani wako ali ndi njala, mupatse chakudya kuti adye; ngati ali ndi ludzu mupatse madzi kuti amwe.


kapena ndi kunama kuti sanatole chinthu chimene chinatayika, kapena kulumbira mwachinyengo pa chinthu chilichonse chimene munthu akachita amachimwa nacho,


Koma Ine ndikuwuzani kuti, ‘Kondani adani anu ndi kuwapempherera okuzunzani


Onetsetsani kuti wina asabwezere choyipa kwa omuchitira choyipa koma nthawi zonse yesetsani kukhala okoma mtima kwa wina ndi mnzake; ndiponso ndi kwa anthu ena onse.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa