Eksodo 23:6 - Buku Lopatulika6 Usakhotetsa mlandu wa mnzako waumphawi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Usakhotetsa mlandu wa mnzako waumphawi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 “Ngati mmodzi mwa anthu ako osauka aimbidwa mlandu, umuweruze molungama ndithu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 “Usakhotetse milandu ya anthu osauka. Onani mutuwo |