Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Eksodo 23:5 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 Ngati uwona bulu wa munthu wina amene amakuda atagwa ndi katundu, usamusiye pomwepo, uwonetsetse kuti wamuthandiza.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

5 Ukaona bulu wa munthu wakudana nawe alikugona pansi ndi katundu wake, ndipo ukadaleka kuthandiza, koma uzimthandiza ndithu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 Ukaona bulu wa munthu wakudana nawe alikugona pansi ndi katundu wake, ndipo ukadaleka kuthandiza, koma uzimthandiza ndithu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Bulu wa mdani wako akagwa ndi katundu, usabzole ndi kumsiya, koma umthandize kuti adzuke.

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 23:5
3 Mawu Ofanana  

Ngati mdani wako ali ndi njala, mupatse chakudya kuti adye; ngati ali ndi ludzu mupatse madzi kuti amwe.


Ngati uwona ngʼombe kapena nkhosa ya mʼbale wako ikusochera, usayilekerere koma uyesetse kuyibwezera kwa iye.


Ngati wapeza bulu kapena ngʼombe ya mʼbale wako itagwa panjira, usayilekerere. Ithandize kuti idzuke.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa