Eksodo 21:9 - Buku Lopatulika9 Koma ngati amtomera mwana wake wamwamuna, amchitire monga kuyenera ana aakazi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Koma ngati amtomera mwana wake wamwamuna, amchitire monga kuyenera ana akazi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Akaganiza zopatsa mwana wake mkaziyo, azidzamsunga ngati mwana wake wamkazi ndithu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Ngati anamusankha kuti akhale mkazi wa mwana wake, ayenera kumusunga ngati mwana wake wamkazi. Onani mutuwo |