Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Eksodo 21:9 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

9 Ngati anamusankha kuti akhale mkazi wa mwana wake, ayenera kumusunga ngati mwana wake wamkazi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

9 Koma ngati amtomera mwana wake wamwamuna, amchitire monga kuyenera ana aakazi.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

9 Koma ngati amtomera mwana wake wamwamuna, amchitire monga kuyenera ana akazi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

9 Akaganiza zopatsa mwana wake mkaziyo, azidzamsunga ngati mwana wake wamkazi ndithu.

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 21:9
2 Mawu Ofanana  

Ngati akwatira mkazi wina, asamumane woyambayo chakudya ngakhale chovala ndipo apiritirize kugona naye ngati mkazi wake.


Koma ngati mkaziyo sakukondweretsa bwana wake amene wamusankha kuti amukwatire, amulole kuti awomboledwe. Bwanayo alibe mphamvu zomugulitsa kwa anthu achilendo, chifukwa iyeyo waphwanya pangano lake lomukwatira iye.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa