Eksodo 20:9 - Buku Lopatulika9 Masiku asanu ndi limodzi uzigwira, ndi kumaliza ntchito zako zonse; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Masiku asanu ndi limodzi uzigwira, ndi kumaliza ntchito zako zonse; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Masiku asanu ndi limodzi uzigwira ntchito zako zonse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Uzigwira ntchito zako zonse masiku asanu ndi limodzi. Onani mutuwo |