Eksodo 20:8 - Buku Lopatulika8 Udzikumbukira tsiku la Sabata, likhale lopatulika. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Udzikumbukira tsiku la Sabata, likhale lopatulika. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 “Uzikumbukira tsiku la Sabata, uzilisunga loyera. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 “Uzisunga tsiku la Sabata kuti likhale lopatulika. Onani mutuwo |
Masiku awa ndinaona ku Yuda ena akuponda mphesa m'choponderamo tsiku la Sabata, ndi akubwera nayo mitolo ya tirigu, ndi kuisenzetsa pa abulu; momwemonso vinyo, mphesa, ndi nkhuyu, ndi zosenza zilizonse, zimene analowa nazo mu Yerusalemu tsiku la Sabata, ndipo ndinawachitira umboni wakuwatsutsa tsikuli anagulitsa zakudya.