Eksodo 2:18 - Buku Lopatulika18 M'mene anafika kwa Reuwele atate wao, iye anati, Mwabwera msanga bwanji lero? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 M'mene anafika kwa Reuwele atate wao, iye anati, Mwabwera msanga bwanji lero? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Atsikana atabwerera kwa bambo wao Reuele, bambo waoyo adaŵafunsa kuti, “Bwanji mwabwerako msanga chotere lero?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Atsikana aja atabwerera kwa abambo awo Reueli, iye anawafunsa kuti, “Chifukwa chiyani lero mwabwera msanga?” Onani mutuwo |