Eksodo 2:17 - Buku Lopatulika17 Pamenepo anadza abusa nawapirikitsa; koma Mose anauka nawathandiza, namwetsa gulu lao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Pamenepo anadza abusa nawapirikitsa; koma Mose anauka nawathandiza, namwetsa gulu lao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Koma kudabwera abusa ena naŵapirikitsa atsikanawo. Apo Mose uja adaimirira naŵathandiza atsikana aja, ndipo adamwetsa zoŵeta zao zonse zija. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Koma kunabwera abusa ena amene anathamangitsa atsikana aja. Ndiye Mose anayimirira nawathandiza atsikana aja ndi kumwetsa nkhosa zawo. Onani mutuwo |