Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Eksodo 2:18 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

18 Atsikana aja atabwerera kwa abambo awo Reueli, iye anawafunsa kuti, “Chifukwa chiyani lero mwabwera msanga?”

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

18 M'mene anafika kwa Reuwele atate wao, iye anati, Mwabwera msanga bwanji lero?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

18 M'mene anafika kwa Reuwele atate wao, iye anati, Mwabwera msanga bwanji lero?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

18 Atsikana atabwerera kwa bambo wao Reuele, bambo waoyo adaŵafunsa kuti, “Bwanji mwabwerako msanga chotere lero?”

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 2:18
7 Mawu Ofanana  

Atsikanawo anayankha kuti, “Mwigupto wina ndiye watilanditsa kwa abusa. Ndiponso anatitungira madzi ndi kumwetsa ziweto zathu.”


Tsono Mose amaweta ziweto za mpongozi wake Yetero, wansembe uja wa ku Midiyani. Tsiku lina iye anazitsogolera kupita ku chipululu ndipo anafika ku phiri la Mulungu lotchedwa Horebu.


Tsono Mose anabwerera kwa Yetero, mpongozi wake ndipo anati kwa Iye, “Chonde ndiloleni kuti ndibwerere ku Igupto kwa anthu anga kuti ndikaone ngati ali moyo.” Yeteri anati, “Pitani mu mtendere.”


Ndipo Mose anawuza Hobabu mwana wa Reueli Mmidiyani, mpongozi wa Mose kuti, “Tikunyamuka kupita ku malo amene Yehova anati, ‘Ndidzakupatsani.’ Tiye upite nafe ndipo tidzakusamalira bwino, pakuti Yehova analonjeza zinthu zabwino kwa Israeli.”


Koma ngati munthu wodetsedwayo sadziyeretsa yekha, ndiye kuti ayenera kuchotsedwa pakati pa gulu chifukwa anadetsa malo wopatulika a Yehova, popeza sanawazidwe madzi oyeretsa ndiye kuti ndi wodetsedwa.


Iwo anamufunsa iye kuti, “Ali kuti munthu ameneyu?” Iye anati, “Ine sindikudziwa.”


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa