Eksodo 18:5 - Buku Lopatulika5 Ndipo Yetero, mpongozi wa Mose, anadza ndi ana ake aamuna ndi mkazi wake kwa Mose kuchipululu kumene adamangako, paphiri la Mulungu; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Ndipo Yetero, mpongozi wa Mose, anadza ndi ana ake amuna ndi mkazi wake kwa Mose kuchipululu kumene adamangako, pa phiri la Mulungu; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Yeteroyo adabwera ndi mkazi wa Mose ndi ana ake aamuna kuchipululu kuja, ku malo amene Mose adamangako mahema, pa phiri la Mulungu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Yetero, mpongozi wa Mose pamodzi ndi ana a Mose aamuna awiri ndi mkazi wake anabwera kwa Mose ku chipululu pa phiri la Mulungu kumene Mose anamanga misasa. Onani mutuwo |