Eksodo 18:6 - Buku Lopatulika6 nati kwa Mose, Ine mpongozi wako Yetero ndadza kwa iwe, ndi mkazi wako, ndi ana ake omwe awiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 nati kwa Mose, Ine mpongozi wako Yetero ndadza kwa iwe, ndi mkazi wako, ndi ana ake omwe awiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Munthu wina adakauza Mose kuti, “Mpongozi wanu Yetero akubwera ndi mkazi wanu ndi ana anu aŵiri aamuna.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Yetero anali atatumiza uthenga kwa Mose kuti, “Ine Yetero, mpongozi wako, ndikubwera ndi mkazi wako ndi ana ake awiri.” Onani mutuwo |